MZIKA ZOKHUDZIDWA M’BOMA LA NENO ZAOPSYEZA NRA PA GANIZO LOSAMUTSA PHULA
Nzika zokhudzidwa m’boma la Neno motsogozedwa ndi phungu waku mpoto kwa bomali a Thoko Tembo zalembera kalata mkulu wa bungwe lowona zamiseu…
Nzika zokhudzidwa m’boma la Neno motsogozedwa ndi phungu waku mpoto kwa bomali a Thoko Tembo zalembera kalata mkulu wa bungwe lowona zamiseu…
Mwana wa Chaka chimodzi ndi miyezi 7 Dennis Polokera Wafa atamugunda ndi galimoto m’boma la Neno. Nneneli wa apolisi ku Neno a…